So Mone

By Yo Maps

Released on November 11, 2023

Thumbnail

[intro: Yo Maps]

Yeah


[verse 1: Yo Maps]

Ati no, permanent, yeah (permanent)

Savuna mwamuna wa permanent (chale, permanent)

Ati nifuna mwamuna wa chizungu

Wama Benz nama mansion

Ali nachuma naka CV

Opunzila naka class

Apa muna kwatilana, so chili bwa?

Nivela mwabwela ku komboni

Naine mulungu, ani sunga

Ninakwatila na tubana

Ninamvela kuti vinasila

Mwamuna wako ni mambala

Sorry-oo, sorry-oo (haibo)


[Chorus: Yo Maps]

Eeh, so, umvela bwangi ukanitamba pa TV yako iwe?

Una sanka mwamuna wa tv not na nzelu, ohh

Muli ine wenzo ona fwaka

Bani tenga bena bo ziba

So mone

So mone-ee

So, umvela bwangi ukanitamba pa tv yako iwe?

Una sanka mwamuna wa Benz not na nzelu, ohh

Muli ine wenzo ona moba

Bani tenga bena bo ziba

So mone

So mone-ee


[verse 2: Tay Grin]

N’akuwuuza, osa meka, ah

Dekha fatsa zidzatheka, ah

Unandisiya chabe wekha

Apa ufuna tibwelеrane

N’akuwuuza, osa meka, ah

Dekha fatsa zidzathеka, ah

Unandisiya chabe wekha

Apa ufuna tibwelerane


[bridge: Tay Grin]

So, chilibwa?

So, chilibwa?

Ndagula nyumba ku 43’

Aa neighbor anga, ndi azungu

Ndalama zanga, ndi za chizungu

So, chilibwa?

So, chilibwa?

Ndagula nyumba ku 43’

Aa neighbor anga, ndi azungu

Ndalama zanga, ndi za chizungu


[Chorus: Yo Maps]

Eeh, so, umvela bwangi ukanitamba pa TV yako iwe?

Una sanka mwamuna wa TV not na nzelu, ohh

Muli ine wenzo ona fwaka

Bani tenga bena bo ziba

So mone

So mone-ee

So, umvela bwangi ukanitamba pa tv yako iwe?

Una sanka mwamuna wa Benz not na nzelu, ohh

Muli ine wenzo ona moba

Bani tenga bena bo ziba

So mone

So mone-ee


[verse 3: Yo Maps]

Ati, hold on

Wamanga bwangi ma nyumba aya?

Baby, hold on

Mukazi wa muchosa kuti, owama uyo?

Ija Benz, nina gula

Mansion, nina manga

Naka CV, nina panga (ahh)


[bridge: Tay Grin]

So, chilibwa?

So, chilibwa?

Ndagula nyumba ku 43

Aa neighbor anga, ndi azungu

Ndalama zanga, ndi za chizungu

So, chilibwa?

So, chilibwa?

Ndagula nyumba ku 43

Aa neighbor anga, ndi azungu

Ndalama zanga, ndi za chizungu


[Chorus: Yo Maps]

So, umvela bwangi ukanitamba pa TV yako iwe?

Una sanka mwamuna wa TV not na nzelu, ohh

Muli ine wenzo ona fwaka

Bani tenga bena bo ziba

So mone

So mone-ee