Released on September 24, 2022

Thumbnail

[Verse 1: Praise Umali]

I worried all the time

I thought I'm running out of time

Can't take it a day at a time sometimes

Man our dreams have been too loud since

We were only young kids

And now, we grown they loud still

I know ndizambiri umafuna mtima

Nde pena mantha ankadzandigwila

Like what if we don't make it (yeah yeah)

What if we don't make it (yeah yeah)


[Chorus: Praise Umali]

Koma tachoka nkutali

Mulungu anali ndi pulani

Pulani

Inu Zonse ndi nthawi

Mulungu anali ndi pulani

Pulani

Yopanga za ifeyo (oooh oooh oooh)

Yopanga za ifeyo

Akupanga za ifeyo (oooh oooh oooh)

Akupanga za ifeyo


[Verse 2: Gwamba]

Yoh

Venue yomweyo ena amaflopa

Samatrenda nyimbo zawo akadropa

Nde pena pride imafuna idzindikopa

Koma mbuye wanga sangakondwe kuti nzizipopa

Nde rule number 1, kumakhala humble

Poti ukazikweza amasiya kupanga zako

Rule number 2, osakhala ndi tsankho

Poti lero ndi kape mawa ali pamwamba pako

Nkayang'ana kumbuyo ngati ndingokuwa mbuye

Ndinakhonza chani kuti inu mundimasule

Mwandichotsa kutali kwinakunso Mulambule

Ulendowu ndiwautali koma


[Chorus: Praise Umali]

Koma tachoka nkutali

Mulungu anali ndi pulani

Pulani

Inu Zonse ndi nthawi

Mulungu anali ndi pulani

Pulani

Yopanga za ifeyo (oooh oooh oooh)

Yopanga za ifeyo

Akupanga za ifeyo (oooh oooh oooh)

Akupanga za ifeyo