[Intro: Beracah]

(DJ Slay)

Oh, yah, yah, yah

[Verse 1: Gwamba & Beracah]

Zambiri yanu ndinamva

Akhungu onse, osamva

Ena osayenda, kungowakhudza inu zawo zinayenda

Nane ndifuna mundikhudze, chonde musandipitilire

Ndatsegula manja, mulore mzimu wanu ukhazikike

Yesu anamva mphavu zikuchoka

Nzimayi wina wake atamugwira

Mavuto ake onse ndikuchoka

Amadwala basi iye ndikuchira

Nane mbuye mundigunde

Mukandiwolotse pamafunde

Ndikudziwa pena ndine nkhutukumve koma mukafuna kukandi-user munde-useh

[Chorus: Beracah]

Mukandikhudza, nyengo zanga zisintha

Mukandikhudza, nyengo zanga

Mumachita zazikulu Yesu ndinamva (Sinkayika konse)

I wanna see your glory, yeah, I wanna testify (Ukulu wanu ndiwuwone)

Koma sindichoka, choka, choka

Mpaka mundikhudze, khudze, khudze

Koma sindichoka, choka, choka

Mpaka mundikhudze, khudze, yeah

[Verse 2: Gwamba]

Mbuye wanga chonde mundikhudze

Ndikalakwitsa chondе mundiwuze

Ndikamachapa chonde mundikhudze

Osalola satana andizunzе

Zolakwika zonse muzichotse

Inu ndi amene mungakonze

Pandekhapa palibe ndingachite nde chonde muzindisamalira nthawi zonse

[Bridge: Gwamba]

Chonde musalole moyo wanga, satana adzalepo zizanga

Chonde musalole Mbuye wanga, satana kulowa in m'moyo

[Chorus: Beracah]

Mukandikhudza, nyengo zanga zisintha

Mukandikhudza, nyengo zanga

Mumachita zazikulu Yesu ndinamva (Sinkayika konse)

I wanna see your glory, yeah, I wanna testify (Ukulu wanu ndiwuwone)

Koma sindichoka, choka, choka

Mpaka mundikhudze, khudze, khudze

Koma sindichoka, choka, choka

Mpaka mundikhudze, khudze, yeah

Mpaka mundikhudze ineyo

Mpaka mundikhudze, yeah