[Chorus: Dan Lu]

Ndayimvela kutali ayi sindigonela ine

Inu Yehova, you're the final say

Matenda angawa ati alibe mamkhwala

Inu Yehova, you're the final say


[Verse 1: Gwamba]

Ay, ambiriwa aku-talker

Akuti ndili ndi tsoka

Ndikamayenda kunyoza

Akuti simundikonda

Akuti ndilibe chuma

Pogona panga pa mphasa

Ayiwala mumalanda

Mukafuna mumapatsa

Tsogolo langa lowala

Ndidakalibe ndi hope

Muzandichotsa ndikukhala

Kukandifikitsa pa top

Muzandiveka zovala

Muzandichotsa manyazi

Muzandipatsa mamkhwala

Matenda onsewa m'madzi


[Chorus: Dan Lu]

Yehova (You're the final say)

Yehova (You're the final say)

Mwandiwona ndine mwana wanu

(You're the final say)

Mundichotse chitonzo papa

(You're the final say)


[Verse 2: Gwamba]

Amangowona kumwamba

Zonsezi mukamakamba

Ndikapempera amanva

Tsiku lina adzayankha

Amangowona kumwamba

Zonsezi mukamakamba

Ndikapempera amanva

Tsiku lina adzayankha


[Bridge: Dan Lu]

Zaka zitatu zadutsa osamuwona mwana ineyo

Anthu akungoseka, anyogodola ati ndine gocho

Koma Yehova (You're the final say)

Misonzi yanga ndapeleka kwa inu

Chitonzo changa muchichotse ndinu

Chimwemwe changa muchiyike ndinu

Ambuye ndalira pa dzina lanu


[Outro: Dan Lu]

(You're the final say)

Yehova (You're the final say)

Mwandiwona ndine mwana wanu (You're the final say)

Munchotse chitonzo baba (You're the final say)

Ahoo (You're the final say)

Yehova (You're the final say)

Ahoo baba (You're the final say)

Ahoo baba (You're the final say)

Final say

Final say

Final say