[Verse 1]

Dear ma hope

Ndalimba mtima lero Sangie

Sindikudziwa zitha bwanji?

Sumandiyankha pa Facebook, Insta, Twitter nanji

Ma bluetick onswewa bwanji?

I've been following you mayi wa ngwiro

Kuyambira Form 1 mpaka 4

Every show ndimakhala konko, sindinajombeko

Sangie, ukundithela bundle


[Chorus]

Kapena mwina chifukwa ndine mwana? Sangie

Sizikugwirizana, Sangie

Mesa tidzikondana

Ndiyankhe njuchi akukakamire

Tell me why?

Tell me why?

Tell me why?

Ndiyankhe Njuchi akukakamire

Tell me why?

Tell me why?

Tell me why?

Ndiyankhe Njuchi akukakamire


[Verse 2]

Tikakumana kwa Sispence

All I get ndi Aire basi

Sangafile Njuchi alibе Viwie

Akatha mtunda ndi minibus

Ndikati ndipemphe sеlfie uli busy

Ndikhole number ili busy

Mayi busy

Still I do it all for love

Ndiyankhe Njuchi aku-, uh


[Chorus]

Kapena mwina chifukwa ndine mwana? Sangie

Sizikugwirizana, Sangie

Mesa tidzikondana

Ndiyankhe Njuchi akukakamire

Tell me why?

Tell me why?

Tell me why?

Ndiyankhe Njuchi akukakamire

Tell me why?

Tell me why?

Tell me why?

Ndiyankhe Njuchi akukakamire

Tell me why?

Tell me why?

Tell me why?

Ndiyankhe Njuchi akukakamire

Tell me why?

Tell me why?

Tell me why?

Ndiyankhe Njuchi akukakamire