The Weeknd

By Crispy Malawi

On Tape II

Released on October 8, 2023

Thumbnail

[Verse 1: Crispy Malawi]

Pomwe Pali Bho-Po ifeso tili pompo (Ifeso tili pompo) (Pompo)

Koma komwe kwavaya gulu lakolo, suzatipeza konko (Sungatipeze konko) (Konko)

Ndili pa easy sindikuyaka, ndangodekha ndungosipper Coco (Ndungosipper Coco) (Coco)

Koma utha ku trappa Baby Gin, Alembe bill yanga pompo (Pa Bill yanga pompo) (Iwe) Olo

Olo Fanta utha ku trappa fukwa ine si Malinga, Ndine Spe-Malawi mfana wama dinkamu

Ndili njapa koma undipeza m'tikamu (Uh huh)

Zisangalalo zodanda ndazitsika

(Huh, Huh, Huh)

Sizimachitika chitika koma leroli zachitika (Hee, Hee, Hee)

Kufewa, kufewa, kufewa ine si Swazi wa Chipika

[Chorus : Crispy Malawi]

Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem

Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game

Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu

Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu

Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja)

Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja)

Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza)

Ma babe anu Sali safe, boys yanga ili outside

[Verse 2 : Krazie G]

From Mzuzu to the Bay, Mad bitches and the lake[?]

Pa denga and the lake, underrated, underpaid

Outdated all these fakes, now it's money over sex

Koma Thako tagwedeza ndiziponya cash ineyo (Ineyo)

Ndiyathu ija, kukonda chills Ndine June, mpasha yama Ninja

Tingoplaya tima tune, yatsa Zaza ija

Ndili chaku moon ndi Hunny wachi figure, Koma ndi singer, andisoka mwina (Mwina)

Kubwera sober pamalo tayakitsa (Tayakitsa)

Tili panja ndi boys ya inside (Inside)

Yang'anitsitsa iyi ndi street fight (Fight), ndizima peace sign

Monalisaaaa (Yeah)

Monalisaaaa (Yeah)

[Chorus : Crispy Malawi & Base Cube]

Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem

Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game

Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu

Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu

Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja)

Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja)

Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza)

Ma Babe anu Sali safe, boys yanga ili (Ayy) (Ayy) (Ayy) outside

[Verse 3 :Base Cube]

Ndi boys tikuchiller Ka, Ku blues tingofila Ka

Olimbana nafe Ali m'madzi tikumwa miller Ka

Spe Wapota reefer ka, uku ndikusipper Ka

Mfana wodelera wakumana nayo Inkata

We livin' a soft life but we go hard with these punches

I'm with the homies mahn so you know some times we get rachet and may leave you in crutches

Koma tayima Kaye tikuchiller Ase

These ladies just want me to tap fukwa ndiku dripper Ase

Ndinafika Ase nde kenako ndinapita ase Ndikuballer opanda keeper Ase

Zi bhawa tikungothila Ase

Spiced up ngati Rajah tadya Zaza Ase, Meek kweza speaker Ase

Weekend sitiyambilatu Friday, utipeza Thursday man tikungofila Aire

Saturday ndili pa easy ndili ndi boys tikuwupeza

Mafana oyera Mtima kukumana pa Zodetsa eish!

[Chorus : Crispy Malawi]

Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem

Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game

Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu

Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu

Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja)

Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja)

Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza)

Ma Babe anu Sali safe, boys yanga ili outside

[Outro]

Cheo Meek Hihihihi Hihihihi