Released on June 10, 2023

Thumbnail

[Intro: Brainlock Jeff Nyimbo & Crispy Malawi]

Mmh hm

(Kotha Kotha) mmh hm (Kotha Kotha)

(Thako thako thako) Gwedeza (Thako thako thako thako thako)

Njanjitsa

(Kotha Kotha) Njanjitsa (Kotha Kotha)

Gwedeza

(Thako thako thako thako thako thako thako)

Who's that[?]

[Chorus: Jeff Nyimbo & Crispy Malawi]

Ubwere pa den ti shoote video (Dance, dance)

Kuvina ngati ukulandira malipiro (Dance dance)

Kuvina slow slow siza liwiro (Dance, dance)

Eya wabwera koma ubweraso litiro?

Gwedeza thako mami Gwedeza (thako)

Njanjitsa thako mami njanjitsa (thako)

Uzindigwira ngati ine ndi (wako)

Ukamanjanjitsa umandipatsa chilakolako


[Verse 1: Crispy Malawi]

Ngati Pali panga iwenso pako

Ndimapanga zanga koma ndipanga zako

Ndikugwira mwendo ndikufinya thako

Lero ndiku punisher ngati ukugwira chibhalo

Body ili tight vibes ndi yambirimbiri

Nde ndikamanyazi kamamasuka kwa awiri (Mmh)

Kamandipatsa for free koma zitha kukwana mili (Mmh)

Or mwina Bili sindudziwa komwe ndili (Mmh)

Trap mami

Ka ku chaser Gin ndi ku chaser money

Mmmh

Tangondipatsa plan

Nditha kudya uh

Nditha kudya plain

[Chorus: Jeff Nyimbo & Crispy Malawi]

Ubwere pa den ti shoote video (Dance, dance)

Kuvina ngati ukulandira malipiro (Dance, dance)

Kuvina slow slow siza liwiro (Dance dancе)

Eya wabwera koma ubweraso litiro?

Gwedеza thako mami Gwedeza (Thako)

Njanjitsa thako mami njanjitsa (Thako)

Uzindigwira ngati ine ndi (Wako)

Ukamanjanjitsa umandipatsa chilakolako


[Verse 2: Jeff Nyimbo]

Umandipatsa chilakolako

Ndikangokhala kuganizira thako lako

Kulikonse chingapite man ndili nacho nacho

Ndizapeza wina akazakhala ndi loposa lako

Ndikaligwira gwira ndimafila

Akatsanzika kupita sindifila

Amadziwa kuphika, kusinja ,ndikuvina

Akayamba sasiya sasiya amangopita


[Outro: Jeff Nyimbo]

Ubwere pa den ti shoote video

Kuvina ngati ukulandira malipiro

Kuvina slow slow siza liwiro

Gwedeza body ngati ma sister pa bwandilo

Gwedeza thako mami Gwedeza thako

Njanjitsa thako mami njanjitsa thako

Uzindigwira ngati ine ndi wako