Step By Step

By Crispy Malawi

On Tape II

Released on September 18, 2023

Thumbnail

[Intro]

Hahaha

Malawian

Ayo

Yeah

It's that time you know


[Chorus]

Step by step tikukwera

Wekha ukuona kuti tikupanga elevate

Ma guy nde asankha kuti azifila Spe

Ena nde ena akuopa akupanga hate

Sleepless nights sakugona

Sapezeke pa poster aka runner tings sitingamupeze

Mutha Kuma hater koma sungadiletse

Mutha Kuma hater koma sungandiletse


[Verse]

Fresh and clean pa chi corner

Kumata pa poster show yo runner ndekha (ndekha)

Homeboy tsitsi wangopota

Tonse tangotchena nde Ena akuti tikupenga

Ndine one of a kind ngati ganja

Iwеyo tangodekha olo abwere ndi yolеnga

Aliyese apa anayamba yekha

Sitinayambile limodzi Ngati liwiro lamu mchenga

Mhu

From zigege to tacos

Ndichi fine Mamie ngati Riana Bagus

Ndinayambira kusuta mibongo

Pano one par yokha imazunguza ubongo

One par itha kukuzunguza ubongo

One par yokha ima zazunguza ubongo

One par yokha itha Kuku zunguza ubongo

One par yokha itha kuzu...mhu Wamva?


[Chorus]

Step by step tikukwera

Wekha ukuona kuti tikupanga elevate

Ma guy nde asankha kuti azifila Spe

Ena nde ena akuopa akupanga hate (hate)

Sleepless nights sakugona

Sapezeke pa poster aka runner tings sitingamupeze

Mutha Kuma hater koma sungadiletse

Mutha Kuma hater koma sungandiletse


[Outro]

Ayo Landie

Mutha Kuma hater koma sungadiletse

Mutha Kuma hater koma sungandiletse

Mutha Kuma hater koma sungandiletse