Released on February 14, 2024

Thumbnail

[Intro: Krazie G & Crispy Malawi]

Tayima Kaye, tayima kaye, tayima kaye tayima kaye, tayima kaye

Ndinabettera success ndiku winner

Ndiku winner, ndikupanga Rebet

Ndilibe Ex Koma ngati Alipo mwina

(Umfila ndani?) amapanga regret

Umafila ndani?

Hahaha


[Chorus: Crispy Malawi]

Ati amafila Spe

Atha kuyimba nyimbo zonse analoweza Tape

Ndangokhala Phee! Ndikufuna ndimumvere

Fanbase yangodzadza ndi ma babe

Boys singasiye kufila Spe

Simangomvera nyimbo imapanga relate

It's all love apapa palibepo hate


[Post-Chorus: Crispy Malawi]

Nde aliyese pamalo pake (Pake, pake, pake, pake, pake)

Aliyese pamalo pake (Pake, pake, pake, pake, pake)

Aliyese pamalo pake (Pake, pake, pake, pake, pake)

Aliyese pamalo pake (Pake, pake, pake, pake, pake)

Aliyese pamalo pake (Pake, pake, pake, pake, pake)

Pake, Pake


[Verse 1 :Crispy Malawi]

Game ili pachi make (Uh-huh), chilichonse chili Malo mwake

Homie Sali stuck koma akufuna ndimukankhe

That's my dawg sangandilume nde sindingamuthawe

Olo ntakhala pa zero iwe dollar sindingakukawe

Bola when I make it double zisazakuwawe

We're on the road tikupanga money ngati katangale

Si zambiri koma zokwana ine ndi A'bale

I don't wanna die before I live my dreams

Lord knows how bad I wanna make these M's

Ku runner game with a milli on my name

Siza Drake koma life was never the same

Pano Ha!


[Chorus: Crispy Malawi]

Ati amafila Spe (Spe!)

(Spe!) Atha kuyimba nyimbo zonse analoweza Tape

Ndangokhala Phee! (Phee!), Ndikufuna ndimumvere (Mvere)

Fanbase yangodzadza ndi ma babe

Boys singasiye kufila Spe

Simangomvera nyimbo imapanga relate

It's all love apa Palibepo hate (Uh huh)


[Post-Chorus: Crispy Malawi]

Nde aliyese pamalo pake (Pake, pake)

Pake, pake, pake, pake (aliyese pamalo pake) pake, pake, pake

Pake, pake, pake, pake, pake, pake, pake

Pake, Pa

Pake, pake, pake, pake, pake, pake, pake

Pake, pa

Pake, pake, pake, pake, pake, pake, pake

Aah!

[Outro: Krazie G & Crispy Malawi]

Ndinabettera success ndiku winner

Ndiku winner ndikupanga Rebet (Je mapelle Spe)

(International Spe) Yeah

Ndilibe Ex koma ngati Alipo

Mwina amapanga regret

Yeah

Brrr! Brrr!

Brrr! Gang!

Brrr! Brrr! Brrr!

Gang, gang, gang

Hahaha

Ndilibe Ex koma ngati Alipo (Malawian)

Mwina amapanga regret

Yeah chilichonse Malo mwake?

Hahaha wakafila bwa?

Ukudziwa kale

Aliyese pamalo pake

Aliyese pamalo pake

Aliyese pamalo pake

Aliyese pa-

Pako

Krazie G