Chibompi

By Crispy Malawi

On DND

Released on June 1, 2024

Thumbnail

[Intro]

It's Nice, it's Nice

Mmh Baby mmh come on

Mmh baby

Ayo Landie

Mmh Mmh mwana salira (Ay-ay, ay-ay)

Mmh Mmh mwana (Ay-ay, ay-ay) salira (Okay-Okay)

Ufuna chani? hmm?


[Chorus]

Chibhompi (Uh-huh, uh-huh)

Mwana akufuna chibompi (Uh-huh)

Mwana akufuna chibompi (Ukufuna chani huh?)

Mwana akufuna chibompi

Nditha kupatsa chimodzi, bola usayambe kudya dothi

Vuto lake kukupatsa chibompi, uyamba kundipatsa chikondi


[Verse 1]

Nde ana ija mafunso ngati uli court

Nali busy kufotokoza zoti "mene umandiwonera muja ineyo tingatayane"

"Iwe chibhompi cha ulere inuyo mungagawane hee?"

Tanena "A" eh Tanena "E" ah wawona?

Nde uziti zandibanda ndikangoyamba kukhafa?

Tiye kubafa yama lover (Uh-Uh-Uh) (Mmh-hm-mmh-hm)


[Chorus]

Chibhompi (Mh hm mh hm)

Mwana akufuna chibompi (Ukufuna chani huh?)

Mwana akufuna chibompi

Mwana akufuna chibompi

Nditha kupatsa chimodzi, bola usayambe kudya dothi

Vuto lake kukupatsa chibhompi, uyamba kundipatsa chikondi


[Verse 2]

Ine kuyiwala zoti ndili ndi mwana man (umatani?)

Kuyamba kukamba zaku Kanapan (Zachamba eti)

Boys kundithila no fireman

Nangotaya man ndili ndi ma man

Ati "Spe usamakonde kusuta chonchi"

Ndampatsa ya banana flavour yapa couch

Nde mix ana amakonda nthochi, kamba puffs ndi chibompi


[Chorus]

Hmm

Chibompi (Uh-uh-uh)

Mwana akufuna chibhompi (akufuna chibompi mwanayi)

Chibompi (Uh-huh)

Mwana akufuna chibompi (Uh-huh, uh-huh)

Nditha kupatsa chimodzi (Eko, Eko) bola usayambe kudya dothi

Vuto lake kukupatsa chibompi uyamba kundipatsa chikondi

Chibompi (Uh-huh)

Mwana akufuna chibompi

'Mwana akufuna chibompi

Mwana akufuna chibompi (Tontholola)


[Outro]

Mwana salira

Eko chibhompi

Eko

We ain't got no time

Mwana wabwino

Mwana wabwino