Released on October 8, 2023

Thumbnail

[Intro]

Cheo Meek

(Kukonda ma bodza)

(Umakonda ma bodza) (Iwe)

(Kukonda ma bodza)

(Umakonda ma bodza) (Ine)

(Kukonda ma bodza)

(Umakonda ma bodza) (Ife)


[Chorus: Crispy Malawi]

Numbers don't lie koma (Bodza ndi labho)

Sindikunamizani guys koma (Bodza ndi labho)

Wapulumuka kangati ase? (Ndibodza lakolo)

Kusekelela za bodza koma kukwiya ndi chilungamo (Ndi chilungamo)

Iwe Numbers don't lie koma (Bodza ndi labho)

Sindikunamizani guys koma (Bodza ndi labho)

Wapulumuka kangati iweyo?

Kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo (Ndi chilungamo)


[Verse 1: Crispy Malawi]

I wish you more life ndi Zi good health

Bodza ndi la bho koma don't lie to yourself

Titalke ma facts bwanji apa uwone ulire

Practice makes perfect sunganame usana chalire

Wamenya call Ku vephi kuti sukufila bho

Ukunama

Mesa umangofuna Ku chilla ndi boys

Out here asking for the truth

Koma you already know

Kuti bodza laku saver wa dodger chilungamo

Pa CV pa dzadza ma bodza (Bodza)

Ma dolo kunamiza ma zoba (Zoba)

Akunama kuti Aku baller (Baller)

Koma Ali padеn kungopola (Bodza)

Koma akuzinamiza okha (Okha)

Ife trap ili makola

(If you love me) Babе chilungamo pena chimazakola

Pena ndimazanama kuti ulipo wekha


[Chorus: Crispy Malawi]

(Bodza ndi labho)

Sindikunamizani guys koma (Bodza ndi labho)

Wapulumuka kangati ase? (Ndibodza lakolo)

Kusekelela za bodza koma kukwiya ndi chilungamo(ndi chilungamo)

Iwe Numbers don't lie koma (Bodza ndi labho)

Sindikunamizani guys koma (Bodza ndi labho)

Wapulumuka kangati iweyo?

Kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo (Ndi chilungamo)


[Verse 2: Virus Infectious]

(Infectious) Ati I love you

Ndili ndi cash a ma bodza a bho

Akazi onsewa Nda bonzapo

Afana ofewa cap ngati wavala chipewa

Koma boys ati ndaba disposable

Ndikuchita kusowa response ya bho

Olo jokes pa mikozi po

Ati dende the boys get toasted

Roasting beats and beef

Of course and some shots been dropping

See the way we run the streets

They dropping off like leaf we smoke them

Got me coughing

Some go deep like the ocean we floating [?]

You know what it is the clan is chosen bro


[Outro: Crispy Malawi]

Don't lie koma (Let's go)

Sindikunamizani guys koma (Let's go)

Wapulumuka kangati ase? (Ndi bodza lako)

Kusekelela za bodza (Ndi chilungamo )

Iwe Numbers don't lie koma

Sindikunamizani guys koma

Wapulumuka kangati iweyo? (Ndi bodza lako)

Kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo (Ndi chilungamo)