Mukunama

By Code Sangala

Released on October 6, 2019

Thumbnail

Mukunama, mukunama,mukunama, mukunama

Kodi ndi ndani ananene kuti onse oyimba ndi anthu osuta fodya

Nanga ndi ndani ananena kuti onse oyimba amangomwa mkala bongo

Mukunama, mukunama,mukunama, mukunama

Tangoganizani moyo wanu ungakhale otani

Patakhala panda nyimbo

Manyado antundu onse amafika pa'nong'a akangothyolapo sound

Mukunama, mukunama,mukunama, mukunama

Mmm,acho,achi

Acho,achi,acho,achi,acho,achi,acho,achi ugwi

Mukunama, mukunama,mukunama, mukunama

Eeh,sure

Ajikandapasye

Eehe,akulambusyatu walakwe

Aaha,ugwi

Aaha,ugwi

Aaha,ugwi

Aaha,ugwi,acho,achi

Sure

Yangali complain baba

Mukunama, mukunama,mukunama, mukunama

Mukunama, mukunama,mukunama, mukunama