Released on December 8, 2023

Thumbnail

[Intro: Base Cube &Crispy Malawi]

Ya

Yeah you know

Hhee Malawian

Mmmh

Yeh, yeh, yeh, yeh, yeh, yeh, yeh, yeh

(Ziwerenge)

(Ziwerenge)


[Verse 1: Crispy Malawi]

Back then, tikuyamba sizinali chonchi tinkangofuna kuheater

Pano tinapita

Ndizopita kuti timangopita

Kufika ngati wa waterboard loza komwe kuli miter

Nfuna kudrippa

Been soft for so long, nthumba mwanga ndikungofuna kulimba


[Hook: Crispy Malawi]

Loza kuli cash ase

Loza kuli cash ase

Loza kuli cash ase


[Verse 2: Crispy Malawi]

Spe uli cold ngati Ice Cube

BT kulinka ndi Base Cube

Views kukwera pa YouTube

Kuplacker zozunguza mutu

DM kwadzaza tinkhuku, utha kusokoneza ndi kududu

Olo utaseka mmakutu, unayamba kundimva Gwamba ali duntu

Back in '018, sanavaye ku area 18

Before i lost my queen, rap isanayembe kupayer rent

Mmutu wanga muli tint

Nsaku runner komwe business

Ma G.O.A.T akupempha ma remix

I had to go and figure it out myself, sungandipusise


[Hook: Crispy Malawi]

Loza kuli cash ase

Loza kuli cash ase

Loza kuli cash ase


[Verse 3: Base Cube]

Yah, mvera

Ndalama zimatikonda, ndkasanja ndimakondwa

Kukhala mmaluzi ukapolo ase, i wanna be freed ngati Honda

Chilichonse timabosha

Look here we ain't got shit on our shoulders

But you know that Im looking for flyer now, man i don't even need a poster

Yah you know that we keep it a hundred, sitidanda tikapeza fifty

Timathamangisa zima business ngati tamva kubwera a city

Ooh yah they callin' me a big dawg, ambirinu mumanditcha biggy

Ndkupanga zindalama zangazanga ndimatchila ndi achina Pisky

Ndimatchila ndi achina Crispy

Pachi weekend, tikusokoneza

Ma guy ambiri amazipopa kaa, ifeyo timangobooleza

Ifey timangobwera kutenga zi cash kutenga zi dollar

Koma ndi mbola mmm

Chifukwa nde tima baller, eyy


[Hook: Base Cube, Crispy Malawi & Base Cube]

Loza kuli cash ase (eyy)

Loza kuli cash ase

Loza kuli cash ase (eyy, iwee)


[Outro: Base Cube]

Malawian