Intro

Yeah

Bizimesi ma Bizimesi

Ma Bizimisi

Ya You know

Haha Malawian

Mmm Hey hey hey

Hey hey hey

Hey hey hey shhh

Zipilinge

Zipilinge

Mmm

Verse 1[Crispy Malawi]

Back then tikuyamba sizidali chonchi

Tinkangofuna kuhita

Pano tinapita ndizopita kuti timangopita

Kufika ngat waterboard loza komwe kuli meter

Funa kudripa Been soft for so long

Nthumba mwanga ndikungofuna kulimba

Hook[Crispy Malawi]

Hey Loza kuli cash Aseh!

Hey Hey

Loza kuli cash Aseh!

Hey Hey

Loza Kuli cash Aseh!

Mmmh Hey Hey ooh!

Verse 2[Crispy Malawi]

SPE uli cold ngat Icecube

Bt Kulinka ndi Basecube

Views kukwera pa YouTube

Kuplugger zozunguza Mutu

Dm kwazaza tinkhuku

Utha kusokoneza ndi ku Dudu

Olo utaseka makutu

Udayamba kundimva Gwamba Ali Duntu

Back no 18

Ndisadavaye ku Area 18

Before I lost my Queen

Rap isadayambe ku payer rent

Mutu mwanga muli tint

Saku runner komwe Business

Ma Goat akupempha ma remix

I had to go and figure it out myself Sungandiputsitse

Hook[Crispy Malawi]

Hey Loza kuli cash Aseh!

Hey Hey

Loza kuli cash Aseh!

Loza Kuli cash Aseh!

Verse 3[Base Cube]

Yea aah vera Ndalama zimandikonda

Ndikasanja ndimakondwa

Kukhala maluzi ukapolo aseh

I wanna be free ngati Honda

Chilichose timabosha

Look we ain't got a chip on our shoulder

But you know that am looking so flyer now, man I don't even need a poster

Yea You know that we keep it a hundred

Sitidanda tikapeza 50

Timathamangisa Zima business ngat tamva kukubwera a City

Oyera calling me a Big Dawg

Ambilinu mumanditcha Biggy

Ndikupanga zindalama zangazanga

Ndimatchila ndi achina Piksy

Ndimatchila ndi achina Crispy

Pachi weekend tikusokoneza

Ma guy ambiri amazipopa ka

Ifeyo timangobowoleza

Ifeyo timangobwera kutenga zi cash kutenga zi dollar

Koma ndi mbola mmm chifukwa nde tima baller iiih eeish iiih eeeh issh ey

Hook[Crispy Malawi & *Basecube* ]

*Eey* Loza kuli cash Aseh!(*Loza Kuli Cash Aseh*)

*Ey*

Loza kuli cash Aseh!(*Loza Kuli Cash Aseh*)

Loza Kuli cash Aseh!(*Loza kuli Cash Aseh*)

*Iweee eey eey*

*Malawian*